20 Cifukwa cace tsono, mwazi wanga usagwe pansi kutati ndi Yehova; pakuti mfumu ya Israyeli yaturuka kudzafuna nsabwe, monga munthu wosaka nkhwali pamapiri.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26
Onani 1 Samueli 26:20 nkhani