1 Samueli 26:23 BL92

23 Ndipo Yehova adzabwezera munthu yense cilungamo cace ndi cikhulupiriko cace, popeza Yehova anakuperekani lero m'dzanja langa, koma sindinalola kutukulira dzanja langa pa wodzozedwa wa Yehova,

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26

Onani 1 Samueli 26:23 nkhani