1 Samueli 28:10 BL92

10 Ndipo Sauli anamlumbirira kwa Yehova, nati, Pali Yehova, palibe cilango cidzakugwera cifukwa ca cinthu ici.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:10 nkhani