11 Comweco Davide analawirira, iye ndi anthu ace, kuti amuke m'mawa ndi kubwera ku dziko la Afilisti. Ndipo Afilisti anakwera ku Jezreeli.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29
Onani 1 Samueli 29:11 nkhani