1 Samueli 3:15 BL92

15 Ndipo Samueli anagona kufikira m'mawa, natsegula zitseko za nyumba ya Yehova. Ndipo Samueli anaopa kudziwitsa Eli masomphenyawo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 3

Onani 1 Samueli 3:15 nkhani