1 Samueli 30:14 BL92

14 Tinathira nkhondo kumwera kwa Akereti ndi ku dziko lija la Ayuda, ndi kumwera kwa Kalebi; ndipo tinatentha mudzi wa Zikilaga ndi moto.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:14 nkhani