1 Samueli 30:16 BL92

16 Ndipo pamene anatsika naye, onani, iwo anabalalika apo ponse, analinkudya, ndi kumwa, ndi kudyerera, cifukwa ca cofunkha zambiri anazitenga ku dziko la Afilisti, ndi ku dziko la Yuda.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:16 nkhani