1 Samueli 30:6 BL92

6 Ndipo Davide anadololoka kwambiri, pakuti anthu ananena za kumponya iye miyala, pakuti mtima wao wa anthu onse unali ndi cisoni, yense cifukwa ca ana ace amuna ndi akazi. Koma Davide anadzilimbikitsa mwa Yehova Mulungu wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:6 nkhani