1 Samueli 30:8 BL92

8 Ndipo Davide anafunsira kwa Yehova, nati, Ndikalondola khamulo ndidzalipeza kodi? Ndipo anamyankha kuti, Lonriola, pakuti zoonadi udzawapeza, ndi kulanditsa zonse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:8 nkhani