1 Samueli 4:1 BL92

1 Ndipo mau a Samueli anafikira kwa Aisrayeli onse. Ndipo Aisrayeli anaturuka kukaponyana nkhondo ndi Afilisti, namanga zithando zao ku Ebenezeri; Afilistiwo namanga m'Afeki.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:1 nkhani