1 Samueli 4:10 BL92

10 Ndipo Afilisti anaponyana nao, nakantha Aisrayeli; iwowa nathawira, munthu yense ku hema wace; ndipo kunali kuwapha kwakukuru; popeza anafako Aisrayeli zikwi makumi atatu a oyenda pansi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:10 nkhani