1 Samueli 4:12 BL92

12 Ndipo munthu wa pfuko la Benjamini anathamanga kucokera ku khamu la ankhondo, nafika ku Silo tsiku lomwelo, ndi zobvala zace zong'ambika, ndi dothi pamutu pace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:12 nkhani