1 Samueli 4:14 BL92

14 Ndipo Eli, pakumva kubuma kwa kulira kwao, anati, Alikupokoseranji? Ndipo munthuyo anafulumira, nadza nauza Eli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:14 nkhani