1 Samueli 4:3 BL92

3 Ndipo pamene anthu anafika ku zithandozo, akuru a Israyeli anati, Yehova anatikanthiranji lero pamaso pa Afilisti? Tikadzitengere likasa la cipangano la Yehova ku Silo, kuti likabwera pakati pa ife, lidzatipulumutsa m'dzanja la adani athu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:3 nkhani