9 Ndipo kunali atafika nalo, dzanja la Yehova linatsutsa mudziwo ndi kusautsa kwakukuru; ndipo anazunza anthu a mudziwo, akuru ndi ang'ono; ndi mafundo anawabuka.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 5
Onani 1 Samueli 5:9 nkhani