1 Samueli 6:12 BL92

12 Ndipo ng'ombezo zinatsata njira yolunjika ku Betisemesi, niziyenda mumseu, zirikulira poyenda; sizinapambukira ku dzanja lamanja, kapena kulamanzere; ndipo mafumu a Afilisti anazitsatira kufikira ku malire a Betisemesi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:12 nkhani