1 Samueli 6:14 BL92

14 Ndipo garetalo linafika m'munda wa Yoswa wa ku Betisemesi, ndi kuima momwemo, pa mwala waukuru; ndipo anawaza matabwa a garetalo, nazipereka ng'ombezo nsembe yopsereza kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:14 nkhani