1 Samueli 8:12 BL92

12 idzawaika akhale otsogolera cikwi, ndi otsogolera makumi asanu; ndipo idzaika ena kulima minda yace, ndi kutema dzinthu zace, ndi kumpangira zipangizo za nkhondo, ndi zipangizo za magareta.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8

Onani 1 Samueli 8:12 nkhani