15 Ndipo idzatenga limodzi la magawo khumi la mbeu zanu, ndi la minda yanu yamphesa, nidzalipatsa akapitao ace, ndi anyamata ace.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8
Onani 1 Samueli 8:15 nkhani