1 Samueli 9:10 BL92

10 Pamenepo Sauli anati kwa mnyamata wace, Wanena bwino; tiye tipite. Comweco iwowa anapita kumudzi kumene kunali munthu wa Mulunguyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:10 nkhani