1 Samueli 9:12 BL92

12 Ndipo anawayankha nati, Alipo; onani ali m'tsogolo mwanu; fulumirani pakuti wabwera lero kumudzi kuno; popeza lero anthu akuti aphere nsembe pamsanje;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:12 nkhani