2 Mafumu 1:15 BL92

15 Pamenepo mthenga wa Yehova anati kwa Eliya, Tsika naye, usamuopa. Nanyamuka iye, natsikira naye kwa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 1

Onani 2 Mafumu 1:15 nkhani