2 Mafumu 1:16 BL92

16 Ndipo ananena nayo, Atero Yehova, Popeza watuma mithenga kukafunsira kwa Baala Zebubu mulungu wa ku Ekroni, kodi ndi popeza palibe Mulungu mwa Israyeli kufunsira mau ace? Cifukwa cace sudzatsika pakama pamene wakwerapo, koma udzafa ndithu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 1

Onani 2 Mafumu 1:16 nkhani