9 Nati Yesaya, Cizindikilo ndici akupatsa Yehova, kuti Yehova adzacicita conena iye; kodi mthunzi umuke m'tsogolo makwerero khumi, kapena ubwerere m'mbuyo makwerero khumi?
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20
Onani 2 Mafumu 20:9 nkhani