2 Mafumu 7:13 BL92

13 Nayankha mmodzi wa anyamata ace, nati, Atenge tsono akavalo otsala asanu, ndiwo otsala m'mudzi; taonani, adzanga unyinji wonse wa Israyeli otsalawo, kapena adzanga unyinji wonse wa Israyeli otsirizika; tiwatumize tione.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:13 nkhani