2 Mafumu 7:14 BL92

14 Motero anatenga magareta awiri ndi akavalo ao; ndipo mfumu inawatumiza alondole khamu la Aaramu, ndi kuti, Mukani mukaone.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:14 nkhani