Miyambi 30:4 BL92

4 Ndani anakwera kumwamba natsikanso?Ndani wakundika nafumbata mphepo?Ndani wamanga madzi m'maraya ace?Ndani wakhazikitsa matsiriziro onse a dziko?Dzina lace ndani? dzina la mwanace ndani? kapena udziwa.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 30

Onani Miyambi 30:4 nkhani