16 iye wakumvera inu, andimvera Ine; ndipo iye wakukana inu, andikana Ine; ndipo iye wakukana Ine amkana iye amene anandituma Ine.
Werengani mutu wathunthu Luka 10
Onani Luka 10:16 nkhani