39 Ndipo anali ndi mbale wace wochedwa Mariya, ndiye wakukhala pa mapazi a Ambuye, namva mau ace.
Werengani mutu wathunthu Luka 10
Onani Luka 10:39 nkhani