18 Ndiponso ngati Satana agawanika kudzitsutsa mwini, udzaimika bwanji ufumu wace? popeza munena kuti nditurutsa ziwanda ndi Beelzebule.
Werengani mutu wathunthu Luka 11
Onani Luka 11:18 nkhani