19 Koma ngati Ine ndimaturutsa ziwanda ndi Beelzebule, ana anu aziturutsa ndi yani? Mwa ici iwo adzakhala oweruza anu.
Werengani mutu wathunthu Luka 11
Onani Luka 11:19 nkhani