15 Ndipo pamene wina wa iwo akuseama pacakudya pamodzi ndi iye anamva izi, anati kwa iye, Wodala iye amene adzadya mkate mu Ufumu wa Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Luka 14
Onani Luka 14:15 nkhani