Luka 15:19 BL92

19 sindiyeneranso konse kuchulidwa mwana wanu; mundiyese ine ngati mmodzi wa anchito anu.

Werengani mutu wathunthu Luka 15

Onani Luka 15:19 nkhani