Luka 16:11 BL92

11 Cifukwa cace ngati simunakhala okhulupirika m'cuma ca cosalungama, adzakhulupirira inu ndani ndi cuma coona?

Werengani mutu wathunthu Luka 16

Onani Luka 16:11 nkhani