1 Ndipo anati kwa ophunzira ace, Sikutheka kuti zolakwitsa zisadze; koma tsoka iye amene adza nazo.
Werengani mutu wathunthu Luka 17
Onani Luka 17:1 nkhani