7 Koma ndani mwa inu ali naye kapolo wolima, kapena woweta nkhosa, amene pobwera iye kucokera kumunda adzanena kwa iye, Lowa tsopano, khala pansi kudya;
Werengani mutu wathunthu Luka 17
Onani Luka 17:7 nkhani