Luka 18:16 BL92

16 Koma Yesu anawaitana, nanena, Lolani ana adze kwa Ine, ndipo musawaletse; pakuti Ufumu wa Mulungu uti wa otere.

Werengani mutu wathunthu Luka 18

Onani Luka 18:16 nkhani