Luka 18:17 BL92

17 Indetu ndinena kwa inu, Ali yense wosalandira Ufumu wa Mulungu ngati mwana, sadzalowamo ndithu.

Werengani mutu wathunthu Luka 18

Onani Luka 18:17 nkhani