14 Koma mfulu za pamudzi pace zinamuda, nizituma akazembe amtsate m'mbuyo ndi kunena, Ife sitifuna munthuyu akhale mfumu yathu.
Werengani mutu wathunthu Luka 19
Onani Luka 19:14 nkhani