Luka 20:10 BL92

10 Ndipo pa nyengo ya zipatso anatumiza kapolo wace kwa olima mundawo, kuti ampatseko cipatso ca mundawo; koma olimawo anampanda, nambweza wopanda kanthu.

Werengani mutu wathunthu Luka 20

Onani Luka 20:10 nkhani