Luka 20:6 BL92

6 ndiponso, tikanena, Ucokera kwa anthu; anthu onse adzatiponya miyala: pakuti akopeka mtima, kuti Yohane ali mneneri.

Werengani mutu wathunthu Luka 20

Onani Luka 20:6 nkhani