11 ndipo kudzakhala zibvomezi zazikuru, ndi njala ndi miliri m'malo akutiakuti, ndipo kudzakhala zoopsya ndi zizindikilo zazikuru zakumwamba.
Werengani mutu wathunthu Luka 21
Onani Luka 21:11 nkhani