10 Ndipo iye anati kwa iwo, Onani, mutalowa m'mudzi, adzakomana ndinu munthu alikusenza mtsuko wa madzi; mumtsate ameneyo kunyumba kumene akalowako iye.
Werengani mutu wathunthu Luka 22
Onani Luka 22:10 nkhani