Luka 22:15 BL92

15 Ndipo anati kwa iwo, Ndinalakalaka ndithu kudya Paskha uwu pamodzi ndinu, ndisanayambe kusautsidwa;

Werengani mutu wathunthu Luka 22

Onani Luka 22:15 nkhani