Luka 22:19 BL92

19 Ndipo m'mene adatenga mkate, nayamika, anaunyema, nawapatsa, nanena, ici ndi thupi langa lopatsidwa cifukwa ca inu; citani ici cikumbukilo canga.

Werengani mutu wathunthu Luka 22

Onani Luka 22:19 nkhani