Luka 22:20 BL92

20 Ndipo coteronso cikho, atatha mgonero, nanena, Cikho ici ndi pangano latsopano m'mwazi wanga wothiridwa cifukwa ca inu.

Werengani mutu wathunthu Luka 22

Onani Luka 22:20 nkhani