Luka 22:8 BL92

8 Ndipo iye anatumiza Petro ndi Yohane, nati, Pitanimutikonzere ife Paskha, kuti tidye.

Werengani mutu wathunthu Luka 22

Onani Luka 22:8 nkhani