22 Ndipo anati kwa iwo nthawi yacitatu, Nanga munthuyu anacita coipa ciani? Sindinapeza cifukwa ca kufera iye; cotero ndidzamkwapula iye ndi kummasula.
Werengani mutu wathunthu Luka 23
Onani Luka 23:22 nkhani