Luka 23:25 BL92

25 Ndipo anawamasulira amene adaponyedwa m'ndende cifukwa ca mpanduko ndi kupha munthu, amene iwo anampempha; koma anapereka Yesu mwa cifuniro cao.

Werengani mutu wathunthu Luka 23

Onani Luka 23:25 nkhani