26 Ndipo popita naye, anagwira munthu, Simoni wa ku Kurene, alikucokera kuminda, namsenza iye mtanda aunyamule pambuyo pace pa Yesu,
Werengani mutu wathunthu Luka 23
Onani Luka 23:26 nkhani